Judges 8:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo sadaonetse mtima wothokoza kwa banja la Yerubaala (ndiye kuti Gideoni), chifukwa cha zabwino zonse zimene iye adaŵachitira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
osachitira chifundo nyumba ya Yerubaala, ndiye Gideoni, monga mwa zokoma zonse iye anachitira Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiponso sanachite zinthu zokomera banja la Yeru-Baala (ndiye kuti Gideoni) chifukwa cha zabwino zonse zimene iye anawachitira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
osacitira cifundo nyumba ya Yerubaala, ndiye Gideoni, monga mwa zokoma zonse iye anacitira Israyeli.