Judges 8:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gideoni adafika ku Yordani naoloka mtsinjewo, iye pamodzi ndi anthu 300 aja amene nali nawo, atatopa kwambiri, koma akupirikitsabe adani ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Gideoni anafika ku Yordani, naoloka, iye ndi amuna mazana atatu anali naye, ali otopa koma ali chilondolere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gideoni anafika ndi kuwoloka mtsinje wa Yorodani pamodzi ndi anthu 300 amene anali naye. Ngakhale kuti anali otopa anapirikitsabe adani awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Gideoni anafika ku Yordano, naoloka, iye ndi amuna mazana atatu anali naye, ali otopa koma ali cilondolere.