Judges 8:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gideoni adayankha kuti, “Ai, chabwino! Chauta akapereka Zeba ndi Zalimuna m'manja mwanga, ndidzakukwapulani ndi matsatsa a minga yam'chipululu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Gideoni anati, Chifukwa chake, Yehova akapereka Zeba ndi Zalimuna m'dzanja langa, ndidzapuntha nyama yanu ndi minga ya m'chipululu ndi mitungwi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gideoni anayankha kuti, “Mwatero! Yehova akapereka Zeba ndi Zalimuna mʼdzanja langa, ndidzakukwapulani ndi matsatsa a minga ya mʼchipululu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Gideoni anati, Cifukwa cace, Yehova akapereka Zeba ndi Tsalimuna m'dzanja langa, ndidzapuntha nyama yanu ndi minga ya m'cipululu ndi mitungwi.