Judges 8:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Gideoni adauza anthu a ku Penuwele kuti, “Pamene ndizikabwerera nditagonjetsa, ndidzagwetsa nsanja ili apayi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananenanso kwa amuna a ku Penuwele ndi kuti, Ndikabwerera ndi mtendere ndidzagumula nsanja iyi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gideoni anawawuzanso kuti, “Ndikamadzabwerera nditawagonjetsa, ndidzagwetsa nsanja iyi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananenanso kwa amuna a ku Penueli ndi kuti, Ndikabwerera ndi mtendere ndidzagumula nsanja iyi.