Judges 9:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Abimeleki, mwana wa Yerubaala, adapita ku Sekemu kwa achibale a mai wake, nakaŵauza iwowo ndi fuko la banja la mai wake kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Abimeleki mwana wa Yerubaala anamuka ku Sekemu kwa abale a amai wake, nanena nao, ndi kwa banja lonse la nyumba ya atate wa amai wake, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abimeleki mwana wa Yeru-Baala anapita ku Sekemu kwa abale a amayi ake ndi kukawawuza iwowo ndi fuko lonse la banja la abambo a amayi ake kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Abimeleki mwana wa Yerubaala anamuka ku Sekemu kwa abale a amai wace, nanena nao, ndi kwa banja lonse la nyumba ya atate wa amai wace, ndi kuti,