Judges 9:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkandankhukuwo udayankha kuti, ‘Ngati mukundidzoza ndi mtima wonse kuti ndikhale mfumu yanu, bwerani mudzabisale mumthunzi mwangamu. Mukapanda kutero, moto utuluke mwa ine ndi kupsereza mikungudza ya ku Lebanoni.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo nkandankhuku unati kwa mitengo, Mukandidzoza mfumu yanu moonadi, tiyeni, thawirani ku mthunzi wanga; mukapanda kutero utuluke moto m'nkandankhuku ndi kunyeketsa mikungudza ya Lebanoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkandankhuku uja unayankha kuti, “Ngati mukufunadi kuti mudzoze ine kuti ndikhale mfumu yanu, bwerani mudzabisale mu mthunzi mwangamu, koma ngati simutero, moto utuluka kwa ine ndi kupsereza mikungudza ya ku Lebanoni.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo nkandankhuku unati kwa mitengo, Mukandidzoza mfumu yanu moonadi, tiyeni, thawirani ku mthunzi wanga; mukapanda kutero uturuke mota m'nkandankhuku ndi kunyeketsa mikungudza ya Lebano.