Judges 9:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Suja bambo wanga adakumenyerani nkhondo naika moyo wake m'zoopsa, kuti akupulumutseni kwa Amidiyani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti atate wanga anakugwirirani nkhondo, nataya moyo wake, nakupulumutsani m'dzanja la Amidiyani;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi suja abambo anga anakumenyerani nkhondo ndi kuyika moyo wawo pa chiswe kuti akupulumutseni mʼmanja mwa Amidiyani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti atate wanga anakugwirirani nkhondo, nataya moyo wace, nakupulumutsani m'dzanja la Amidyani;