Judges 9:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati sizili choncho, moto utuluke mwa Abimeleki, upsereze nzika za ku Sekemu pamodzi ndi anthu a ku nyumba ya Betemilo. Ndipo moto utuluke mwa nzika za ku Sekemu ndiponso mwa anthu a ku nyumba ya Betemilo ndi kupsereza Abimeleki.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma ngati simunatero, utuluke moto kwa Abimeleki, nunyeketse eni ake a ku Sekemu ndi nyumba ya Milo; nutuluke moto kwa eni ake a ku Sekemu, ndi kunyumba yake ya Milo, nunyeketse Abimeleki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati sichoncho moto utuluke mwa Abimeleki ndi kupsereza anthu a ku Sekemu ndi Beti-Milo, ndipo moto utulukenso mwa anthu a ku Sekemu ndi Beti-Milo, ndi kupsereza Abimeleki!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma ngati simunatero, uturuke moto kwa Abimeleki, nunyeketse eni ace a ku Sekemu ndi nyumba ya Milo; nuturuke mota kwa eni ace a ku Sekemu, ndi ku nyumba yace ya Milo, nunyeketse Abimeleki.