Judges 9:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yotamu adathaŵa napita ku Beere ndipo adakakhala komweko, kuwopa Abimeleki mbale wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yotamu anafulumira, nathawa, namuka ku Beere, nakhala komweko, chifukwa cha Abimeleki mbale wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yotamu anathawira ku Beeri nakakhala komweko chifukwa ankaopa Abimeleki mʼbale wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yotamu anafulumira, nathawa, namuka ku Beeri, nakhala komweko, cifukwa ca Abimeleki mbale wace.