Judges 9:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adaika chidani pakati pa Abimeleki ndi anthu a ku Sekemu, ndipo anthu a ku Sekemuwo adamuukira Abimeleki.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu anatumiza mzimu woipa pakati pa Abimeleki ndi eni ake a ku Sekemu; ndi eni ake a ku Sekemu anamchitira Abimeleki mosakhulupirika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu anayika chidani pakati pa Abimelekiyo ndi anthu a ku Sekemu, motero kuti anthu a ku Sekemu anawukira Abimeleki.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu anatumiza mzimu woipa pakati pa Abimeleki ndi eni ace a ku Sekemu; ndi eni ace a ku Sekemu anamcitira Abimeleki mosakhulupirika;