Judges 9:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina Gaala, mwana wa Ebedi, adasamukira ku Sekemu pamodzi ndi achibale ake. Ndipo anthu a ku Sekemu adamkhulupirira iyeyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Gaala, mwana wa Ebedi anadza ndi abale ake, napita ku Sekemu; ndi eni ake a ku Sekemu anamkhulupirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gaali mwana wa Ebedi anasamukira ku Sekemu ndi abale ake, ndipo anthu a ku Sekemuko anamukhulupirira iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Gaala, mwana wa Ebedi anadza ndi abale ace, napita ku Sekemu; ndi eni ace a ku Sekemu anamkhulupirira.