Judges 9:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amumzindamu akadakhala pansi pa ulamuliro wanga, bwenzi nditamchotsa Abimelekiyo, ndipo ndikadamuuza kuti, ‘Onjezera ankhondo ako ndipo bwera, timenyane nkhondo.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwenzi anthu awa akadakhala m'dzanja langa; ndikadamchotsadi Abimeleki. Ndipo anati kwa Abimeleki, Chulukitsa khamu lako, nutuluke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a mu mzindawo akanakhala pansi pa ulamuliro wanga, ndikanamuchotsa Abimelekiyu. Ndikanamuwuza Abimeleki kuti, ‘Wonjeza ankhondo ako ndipo ubwere tidzamenyane!’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwenzi anthu awa akadakhala m'dzanja langa; ndikadamcotsadi Abimeleki. Ndipo anati kwa Abimeleki, Curukitsa khamu lako, nuturuke.