Judges 9:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Achibale a mai wakewo adamlankhulirako kwa anthu onse a ku Sekemu ndipo mitima yao ya anthuwo inali pa Abimeleki pakuti ankati, “Ameneyu ndi mbale wathu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo abale a amake anamnenera mau awa onse m'makutu a eni ake onse a Sekemu; ndi mitima yao inalunjika kutsata Abimeleki; pakuti anati, Ndiye mbale wathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale a amayi akewo anamuyankhulira mawu amenewa kwa nzika zonse za ku Sekemu, ndipo mitima ya anthu onse inali pa Abimeleki chifukwa anati, “Uyu ndi mʼbale wathu,”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo abale a amace anamnenera mau awa onse m'makutu a eni ace onse a Sekemu; ndi mitima yao inalunjika kutsata Abimeleki; pakuti anati, Ndiye mbale wathu.