Judges 9:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Zebuli, munthu wolamulira mzindawo, adamva mau a Gaala mwana wa Ebedi, adapsa mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene Zebuli woyang'anira mudzi anamva mau a Gaala mwana wa Ebedi, anapsa mtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zebuli amene ankalamulira mzindawo atamva zimene Gaali mwana wa Ebadi ananena, anakwiya kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene Zebuli woyang'anira mudzi anamva mau a Gaala mwana wa Ebedi, anapsa mtima.