Judges 9:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatuma amithenga kwa Abimeleki ku Aruma kukanena kuti, “Gaala, mwana wa Ebedi, pamodzi ndi achibale ake, abwera ku Sekemu, akuutsa mitima ya anthu mu mzinda kuti akuukireni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natuma mithenga kwa Abimeleki ku Aruma monyenga nati, Taonani Gaala mwana wa Ebedi ndi abale ake afika ku Sekemu; ndipo taonani, akupandukitsirani mudzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anatumiza amithenga kwa Abimeleki, kukanena kuti, “Gaali mwana wa Ebedi ndi abale ake abwera ku Sekemu ndipo akuwutsa mitima ya anthu a mu mzindawo kuti akuwukireni inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Natuma mithenga kwa Abimeleki monyenga nati, Taonani Gaala ndi abale ace afika ku Sekemu; ndipo taonani, akupandukitsirani mudzi.