Judges 9:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gaala adalankhulanso nati, “Ona, anthu akutsika kuchokera pakati penipeni pa phiri, ndipo gulu limodzi likuchokera mbali ya ku mtengo wa thundu wa amaula.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Gaala ananenanso, nati, Tapenya alikutsika anthu pakati pa dziko, ndi gulu limodzi lidzera njira ya ku thundu wa alauli.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Gaaliyo anayankhulanso kuti, “Taona anthu akutsika kuchokera pakati pa phiri, ndipo gulu lina likubwera kuchokera ku mtengo wa thundu wa owombeza mawula.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Gaala ananenanso, nati, Tapenya alikutsika anthu pakati pa dziko, ndi gulu limodzi lidzera olira ya ku thundu wa alauli.