Judges 9:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa mwake anthu a ku Sekemu adapangana kuti apite ku minda, ndipo Abimeleki adazimva zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali m'mawa mwake, kuti anthu anatuluka kunka kuminda; ndipo anauza Abimeleki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa mwake anthu a ku Sekemu anapangana zopita ku minda, ndipo Abimeleki anamva zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali m'mawa mwace, kuti anthu anaturuka kumka kuminda; ndipo anauza Abimeleki.