Judges 9:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adatenga anthu ake, adaŵagaŵa m'magulu atatu, nakabisala m'minda. Ataona anthu akutuluka mu mzinda, pompo adapita kukalimbana nawo, naŵapha onsewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anatenga anthu, nawagawa magulu atatu, nalalira m'minda; napenya, ndipo taonani, anthu alimkutuluka m'mudzi; nawaukira iye nawakantha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Abimeleki anatenga anthu ake, nawagawa magulu atatu ndi kukabisala mʼminda. Ataona anthu akutuluka mu mzindawo, iye anapita kukalimbana nawo ndipo onsewo anawapha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anatenga anthu, nawagawa magulu atatu, nalalira m'minda; napenya, ndipo taonani, anthu alimkuturuka m'mudzi; nawaukira iye nawakantha.