Judges 9:46 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onse a ku nsanja ya Sekemu atamva zimenezo, adakaloŵa m'linga la nyumba yachipembedzo ya Baala wa Chipangano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene eni ake onse a nsanja ya ku Sekemu anachimva, analowa m'ngaka ya nyumba ya Eliberiti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a mu nsanja ya Sekemu atamva zimenezi, anakalowa mu linga la nyumba yopembedzeramo Baala-Beriti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene eni ace onse a nsanja ya ku Sekemu anacimva, analowa m'ngaka ya nyumba ya Eliberiti.