Judges 9:47 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abimeleki adazimva zakuti anthuwo asonkhana kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anauza Abimeleki kuti amuna onse a nsanja ya ku Sekemu asonkhane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abimeleki anamva kuti anthu ena asonkhana kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anauza Abimeleki kuti amuna onse a nsanja ya ku Sekemu asonkhane.