Judges 9:51 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumzindawo munali nsanja yolimba, ndipo anthu onse amumzindamo, amuna onse ndi akazi omwe, adathaŵira m'nsanjamo, nadzitsekera m'kati. Ndipo adakwera ku tsindwi la nsanjayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma m'mudzimo munali nsanja yolimba nathawira kumeneko amuna ndi akazi onse, ndi eni ake onse a mudziwo, nadzitsekereza m'mwemo, nakwera patsindwi pa nsanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mu mzindamo munali nsanja yolimba. Anthu onse a mu mzindamo amuna ndi akazi anathawira mu nsanjayo, nadzitsekera mʼkati. Ndipo anakwera ku denga la nsanjayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma m'mudzimo munali nsanja yolimba nathawira kumeneko amuna ndi akazi onse, ndi eni ace onse a mudziwo, nadzitsekereza m'mwemo, nakwera patsindwi pa nsanja.