Judges 9:52 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abimeleki adabwera ku nsanja ija, naithira nkhondo, ndipo adakafika pafupi ndi chitseko cha nsanjayo kuti achitenthe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abimeleki anafika kunsanja, nalimbana nayo nkhondo, nayandikira kukhomo kwa nsanja, aitenthe ndi moto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abimeleki anapita ku nsanjayo nathira nkhondo. Anafika pafupi ndi chitseko cha nsanja ija kuti ayitenthe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abimeleki anafika kunsania, nalimbana nayo nkhondo, nayandikira kukhomo kwa nsanja, aitenthe ndi moto.