Judges 9:53 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mkazi wina wake adaponya mwala wa mphero pa mutu wa Abimeleki, nautswanya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mkazi wina anaponya mwana wa mphero pamutu pa Abimeleki, naphwanya bade lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mkazi wina anaponya mwala wa mphero pa mutu wa Abimeleki ndi kuswa chibade cha mutuwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mkazi wina anaponya mwana wa mphero pamutu pa Abimeleki, naphwanya bade lace.