Judges 9:55 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele ataona kuti Abimeleki wafa, onse adapita kwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene amuna a Israele anaona kuti adafa Abimeleki anamuka yense kumalo kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli ataona kuti Abimeleki wafa, anapita kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene amuna a Israyeli anaona kuti adafa Abimeleki anamuka yense kumalo kwace.