Judges 9:57 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adaŵalanganso anthu a ku Sekemu chifukwa cha kuipa kwao, ndipo matemberero aja a Yotamu, mwana wa Yerubaala, adaŵagweradi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mulungu anawabwezera choipa chonse cha amuna a ku Sekemu pamitu pao, ndipo linawagwera temberero la Yotamu mwana wa Yerubaala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu anawalanganso anthu a ku Sekemu chifukwa cha kuyipa kwawo konse. Ndipo matemberero a Yotamu mwana wa Yeru-Baala anawagweradi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mulungu anawabwezera coipa conse ca amuna a ku Sekemu pamitu pao, ndipo linawagwera temberero la Yotamu mwana wa Yerubaala.