Lamentations 1:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ziyoni wakweza manja, koma palibe ndi mmodzi yemwe womusangalatsa. Chauta adalamula kuti Yakobe anansi ake asanduke adani ake. Yerusalemu wasanduka chinthu chonyansa pakati pao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ziyoni atambasula manja ake, palibe wakumtonthoza; Yehova walamulira kuti omzungulira Yakobo akhale adani ake; Yerusalemu wasanduka chinthu chonyansa pakati pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ziyoni wakweza manja ake, koma palibe aliyense womutonthoza. Yehova walamula kuti abale ake a Yakobo akhale adani ake; Yerusalemu wasanduka chinthu chodetsedwa pakati pawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ziyoni atambasula manja ace, palibe wakumtonthoza; Yehova walamulira kuti omzungulira Yakobo akhale adani ace; Yerusalemu wasanduka cinthu conyansa pakati pao.