Lamentations 1:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Chauta wakhoza, chifukwa ndine ndidapandukira malamulo ake. Imvani, inu anthu a mitundu yonse, onani kuvutika kwanga. Anamwali anga ndi anyamata anga atengedwa ukapolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ali wolungama; pakuti ndapikisana ndi m'kamwa mwake; mumvetu, mitundu ya anthu nonsenu, nimuone chisoni changa; anamwali ndi anyamata anga atha kulowa m'ndende.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova ndi wolungama, koma ndine ndinawukira malamulo ake. Imvani inu anthu a mitundu yonse; onani masautso anga. Anyamata ndi anamwali anga agwidwa ukapolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ali wolungama; pakuti ndapikisana ndi m'kamwa mwace: Mudtvetu, mitundu ya anthu nonsenu, nimuone cisoni canga; Anamwali ndi anyamata anga atha kulowa m'ndende.