Lamentations 1:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidaitana abwenzi anga, koma iwo adanditaya. Ansembe anga ndi akuluakulu anga adafa mu mzinda, pamene ankafunafuna chakudya kuti mphamvu zao zibwereremo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinaitana akundikondawo koma anandinyenga; ansembe ndi akulu anga anamwalira m'mudzimu, alikufunafuna zakudya zotsitsimutsa miyoyo yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndinayitana abwenzi anga koma anandinyenga. Ansembe ndi akuluakulu anga anafa mu mzinda pamene ankafunafuna chakudya kuti akhale ndi moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinaitanaakundikondawokoma anandinyenga; Ansembe ndi akulu anga anamwalira m'mudzimu, Alikufunafuna zakudya zotsitsimutsa miyoyo yao.