Lamentations 3:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndine munthu amene ndaona mavuto, ndalangidwa ndi ndodo ya ukali wa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine ndine munthuyu wakuona msauko ndi ndodo ya ukali wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndine munthu amene ndaona masautso ndi ndodo ya ukali wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine ndine munthuyu wakuona msauko ndi ndodo ya ukali wace.