Lamentations 3:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adalasa mtima wanga ndi mivi ya m'phodo lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Walasa impso zanga ndi mivi ya m'phodo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Walasa mtima wanga ndi mivi ya mʼphodo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Walowetsa m'imso mwanga mibvi ya m'phodo mwace.