Lamentations 3:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandigulula mano ndi timiyala, adandivimviniza m'phulusa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wathyolanso mano anga ndi tinsangalabwi, wandikuta ndi phulusa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wathyola mano anga ndi miyala; wandiviviniza mʼfumbi;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Watyolanso mano anga ndi tinsangalabwi, wandikuta ndi phulusa.