Lamentations 3:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimakumbukira masautso anga ndi kuzunzika kwanga, zili ngati chivumulo ndi ndulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumbukirani msauko wanga ndi kusochera kwanga, ndizo chivumulo ndi ndulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kukumbukira masautso anga ndi kusowa pokhala, zili ngati zowawa ndi ndulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumbukirani msauko Wanga ndi kusocera kwanga, ndizo civumulo ndi ndulu.