Lamentations 3:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa mulimonse zachifundozo zimaoneka zatsopano, chifukwa Chauta ndi wokhulupirika kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chioneka chatsopano m'mawa ndi m'mawa; mukhulupirika ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimaoneka zatsopano mmawa uliwonse; kukhulupirika kwanu nʼkwakukulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cioneka catsopano m'mawa ndi m'mawa; mukhulupirika ndithu.