Lamentations 3:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithudi Ambuye sadzataya atumiki ao mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova sadzataya kufikira nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa Ambuye satayiratu anthu nthawi zonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova sadzataya kufikira nthawi zonse,