Lamentations 3:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Savutitsa mwadala, sakonda kusautsa munthu aliyense.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti samasautsa dala, ngakhale kumvetsa ana a anthu chisoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti sabweretsa masautso mwadala, kapena zowawa kwa ana a anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti samasautsa dala, ngakhale kumvetsa ana a anthu cisoni.