Lamentations 3:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndani angathe kulamula kuti zakutizakuti zichitike, ngati Chauta waletsa zimenezo?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndani anganene, chonena chake ndi kuchitikadi, ngati Ambuye salamulira?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndani angayankhule zinthu nʼkuchitika ngati Ambuye sanavomereze?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndani anganene, conena cace ndi kucitikadi, ngati Ambuye salamulira?