Lamentations 3:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wina aliyense wamoyo angadandaulirenji pamene alangidwa chifukwa cha machimo ake?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi munthu wamoyo adandauliranji pokhala m'zochimwa zake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi nʼchifukwa chiyani munthu aliyense wamoyo amadandaula akalangidwa chifukwa cha machimo ake?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi munthu wamoyo adandauliranji pokhala m'zocimwa zace?