Lamentations 3:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tikweze mitima yathu ndi manja athu kwa Mulungu kumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Titukulire mitima yathu ndi manja athu omwe kwa Mulungu ali kumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tiyeni tikweze mitima yathu ndi manja athu kwa Mulungu kumwamba ndipo tinene kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Titukulire mitima yathu ndi, manja athu omwe kwa Mulungu ali kumwamba.