Lamentations 3:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maso mwanga misozi ikungoti mbwembwembwe, chifukwa anthu anga aonongeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'diso mwanga mutsika mitsinje ya madzi chifukwa cha mwana wamkazi wa anthu a mtundu wanga woonongedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Misozi mʼmaso mwanga ikungoti mbwembwembwe chifukwa anthu anga akuwonongedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'diso mwanga mutsikamitsinje ya madzi cifukwa ca mwana wamkazi wa anthu amtundu wanga woonongedwa,