Lamentations 3:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandizinga ndi kundizunguliza ponseponse ndi mazunzo ndi masautso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wandimangira zithando za nkhondo, wandizinga ndi ulembe ndi mavuto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wandizinga ndi kundizungulira ndi zowawa ndi zolemetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wandimangira zitando za nkhondo, wandizinga ndi ulembe ndi mabvuto.