Lamentations 3:51 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga ukupweteka poona zimene zikuŵachitikira akazi a mumzinda mwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Diso langa limvetsa moyo wanga zowawa chifukwa cha ana akazi onse a m'mudzi mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wanga ukupweteka poona zimenezi chifukwa cha akazi onse a mu mzinda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Diso langa limvetsa moyo wanga zowawa cifukwa ca ana akazi onse a m'mudzi mwanga.