Lamentations 3:54 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Madzi adaamiza mutu wanga, ine nkunena ku, “Mayo, ndikufa ine!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
madzi anayenda pamwamba pa mutu panga, ndinati, Ndalikhidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
madzi anamiza mutu wanga ndipo ndinkaganiza kuti imfa yayandikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Madzi anayenda pamwamba pa mutu panga, ndinati, dalikhidwa.