Lamentations 3:55 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidatama dzina lanu mopemba, Inu Chauta, ndili m'dzenje lozamalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinaitana dzina lanu, Yehova, ndili m'dzenje lapansi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinayitana dzina lanu Inu Yehova, kuchokera mʼdzenje lozama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinaitana dzina lanu, Yehova, ndiri m'dzenje lapansi;