Lamentations 3:56 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mudamva mau anga akuti, “Musagonthetse dala makutu anu pamene ndikupemphera kuti mudzandithandize.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
munamva mau anga; musabise khutu lanu popuma ndi pofuula ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munamva kudandaula kwanga. “Mundimvere kulira kwanga kopempha thandizo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munamva mau anga; musabise khutu lanu popuma ndi popfuulaine.