Lamentations 3:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanditaya m'malo a mdima wabii, kuti ndikhale ngati munthu wofa kalekale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wandikhalitsa mumdima ngati akufa kale.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wandikhazika mu mdima ngati amene anafa kale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wandikhalitsa mumdima ngati akufakale.