Lamentations 3:63 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onani m'mene akundinyozera, m'maŵa ndi madzulo akungokhalira kundiimba nyimbo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani kukhala ndi kunyamuka kwao; ndine nyimbo yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tawaonani! Kaya ali pansi kapena kuyimirira, akundinyoza mu nyimbo zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani kukhala ndi kunyamuka kwao; ndine nyimbo yao.