Lamentations 3:64 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, muŵalange potsata zolakwa zao, potsata ntchito zimene adachita.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzawabwezera chilango, Yehova, monga mwa machitidwe a manja ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova, muwabwezere chowayenera, chifukwa cha zimene manja awo achita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzawabwezera cilango, Yehova, monga mwa macitidwe a manja ao;