Lamentations 3:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanditsekera m'malinga kuti ndisathaŵe. Adandimanga ndi maunyolo olemera kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wanditsekereza ndi guta, sindingatuluke; walemeretsa unyolo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wandimangira khoma kotero kuti sindingathawe, wandimanga ndi maunyolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wanditsekereza ndi guta, sindingaturuke; walemeretsa unyolo wanga.