Lamentations 4:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ha! Golide wathu tsopano wathimbirira kwambiri. Golide wathu wosalala uja wasinthika kotheratu. Miyala ya ku malo oyera yamwazikana, ili vuu, ku mphambano zonse za miseu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ha! Golide wagugadi; golide woona woposa wasandulika; miyala ya malo opatulika yakhuthulidwa pa malekezero a makwalala onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Haa! Golide wathimbirira, golide wosalala wasinthikiratu! Amwazamwaza miyala yokongola ya kumalo opatulika pamphambano ponse pa mzinda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ha! golidi wagugadi; golidi woona woposa wasandulika; Miyala ya malo opatulika yakhutulidwa pa malekezero a makwalalaonse.