Lamentations 4:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafumu a pa dziko lapansi sadakhulupirire, kapena wina aliyense wokhala pa dziko lapansi, kuti adani kapena ankhondo nkuloŵa pa zipata za Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mafumu a dziko lapansi sanakhulupirire, ngakhale onse okhala kunja kuno, kuti adani ndi amaliwongo adzalowadi m'zipata za Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mafumu a pa dziko lapansi sanakhulupirire, kapena wina aliyense wokhala pa dziko lonse, kuti adani kapena ankhondo akhoza kulowa pa zipata za Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mafumu a dziko lapansi sanakhulupirira, ngakhale onse okhala kunja kuno, Kuti adani ndi amaliwongo adzalowadi m'zipata za Yerusalemu.